Numbers 33:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Mitika, nakamanga mahema ao ku Hasimona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nachokera ku Mitika, nayenda namanga m'Hasimona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Mitika anakamanga ku Hasimona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nacokera ku Mitika, nayenda namanga m'Hasimona.