Numbers 33:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanga mahema ao pafupi ndi mtsinje wa Yordani kuyambira ku Beteyesimoti mpaka ku Abele-Sitimu, m'zigwa za Mowabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamanga pa Yordani, kuyambira ku Beteyesimoti kufikira ku Abele-Sitimu m'zidikha za Mowabu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ali ku zigwa za Mowabu anamanga mʼmbali mwa Yorodani kuchokera ku Beti-Yesimoti mpaka ku Abeli-Sitimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamanga pa Yordano, kuyambira ku Beti Yesimoti kufikira ku Abeli Sitimu m'zidikha za Moabu.