Numbers 33:51 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti, Pamene muwoloka mtsinje wa Yordani kuti muloŵe m'dziko la Kanani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mutaoloka Yordani kulowa m'dziko la Kanani,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nena kwa Aisraeli kuti, ‘Pamene muwoloka Yorodani kulowa mʼdziko la Kanaani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mutaoloka Yordano kulowa m'dziko la Kanani,