Numbers 33:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzalande dzikolo kuti likhale lanu, ndipo mudzakhale m'menemo, poti ndakupatsani kuti likhale lanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo mulande dziko, ndi kukhala m'mwemo, pakuti ndinakupatsani inu dzikoli likhale lanulanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukalande dzikolo ndi kukhalamo chifukwa ndakupatsani dziko limenelo kuti mukhalemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo mulande dziko, ndi kukhala m'mwemo, pakuti ndinakupatsani inu dzikoli likhale lanu lanu.