Numbers 33:56 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidzakuchitani inuyo zimene ndinkaganiza kuti ndiŵachite iwowo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzakhala kuti monga ndinayesa kuchitira iwowa, ndidzakuchitirani inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pamenepo ndidzachitira inu zomwe ndinaganiza kuwachitira iwowo.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzakhala kuti monga ndinayesa kucitira iwowa, ndidzakucitirani inu.