Numbers 33:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Sukoti nakamanga mahema ku Etamu, mzinda umene uli m'mbali mwa chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nachokera ku Sukoti, nayenda namanga m'Etamu, ndiko ku malekezero a chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Sukoti anakamanga misasa yawo ku Etamu, mʼmbali mwa chipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nacokera ku Sukoti, nayenda namanga m'Etamu, ndiko ku malekezero a cipululu.