Numbers 33:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanyamuka ku Mara nakafika ku Elimu. Ku Elimuko kunali akasupe khumi ndi aŵiri ndi mitengo ya migwalangwa makumi asanu ndi aŵiri, ndipo adamanga mahema ao kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachokera ku Mara, nayenda nafika ku Elimu, ku Elimu ndiko kuli akasupe khumi ndi awiri a madzi, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; namanga iwo komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atachoka ku Mara anafika ku Elimu, kumene kunali akasupe a madzi khumi ndi awiri ndi mitengo ya migwalangwa 70 ndipo anamanga misasa yawo kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacokera ku Mara, nayenda nafika ku Elimu, ku Elimu ndiko kuli akasupe khumi ndi awiri a madzi, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; namanga iwo komweko.