Numbers 34:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mulembe malire anu akuvuma kuyambira ku Hazarenaniko mpaka ku Sefamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzilembere malire a kum'mawa ochokera ku Hazara-Enani kunka ku Sefamu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Za malire anu a kummawa, mulembe mzere kuchokera ku Hazari-Enani mpaka kukafika ku Sefamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzilembere malire a kum'mawa ocokera ku Hazara Enani kumka ku Sefamu;