Numbers 34:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Fuko la ana a Rubeni mwa mabanja a makolo ao, ndi fuko la ana a Gadi mwa mabanja a makolo ao, pamodzi ndi theka la fuko la Manase, adalandira kale choloŵa chao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza fuko la ana a Rubeni monga mwa nyumba za makolo ao, ndi fuko la ana a Gadi monga mwa nyumba za makolo ao, adalandira, ndi fuko la hafu la Manase lalandira cholowa chao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa mabanja a fuko la Rubeni, fuko la Gadi, ndi theka la fuko la Manase analandiriratu cholowa chawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popeza pfuko la ana a Rubeni monga mwa nyumba za makolo ao, ndi pfuko la ana a Gadi monga mwa nyumba za makolo ao, adalandira, ndi pfuko la hafu la Manase lalandira colowa cao;