Numbers 34:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mutenge mtsogoleri mmodzi pa fuko lililonse, kuti agaŵe dzikolo ngati choloŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku fuko limodzi, agawe dziko likhale cholowa chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musankhe mtsogoleri mmodzi kuchokera ku fuko lililonse kuti athandize kugawa dzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku pfuko limodzi, agawe dziko likhale colowa cao.