Numbers 34:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maina a anthuwo naŵa: M'fuko la Yuda akhale Kalebe mwana wa Yefune.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maina a amunawo ndiwo: wa fuko la Yuda, Kalebe mwana wa Yefune.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayina awo ndi awa: Kalebe mwana wa Yefune, wochokera ku fuko la Yuda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maina a amunawo ndiwo: wa pfuko la Yuda, Kalebi mwana wa Yefune.