Numbers 34:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ulamule Aisraele, uŵauze kuti, ‘Posachedwa muloŵa m'dziko la Kanani, (dziko limenelo ndilo lidzakhala choloŵa chanu, dziko lonse la Kananilo).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uza ana a Israele, nunene nao, Mutalowa m'dziko la Kanani, ndilo dziko logwera inu, likhale cholowa chanu, dziko la Kanani monga mwa malire ake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Lamula Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Pamene mulowa mʼdziko la Kanaani, dziko lomwe lidzaperekedwa kwa inu ngati cholowa chanu, lidzakhale ndi malire awa:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uza ana Israyeli, nunene nao, Mutalowa a m'dziko la Kanani, ndilo dziko logwera inu, likhale colowa canu, dziko ija Kanani monga mwa malire ace,