Numbers 34:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'fuko la ana a Dani akhale Buki mwana wa Yogili.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa fuko la ana a Dani, kalonga Buki mwana wa Yogili.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Buki mwana wa Yogili, mtsogoleri wochokera ku fuko la Dani;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa pfuko la ana a Dani, kalonga Buki mwana wa Yogili.