Numbers 34:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa ana a Yosefe, m'fuko la ana a Manase akhale Haniyele mwana wa Efodi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hanieli mwana wa Efodi, mtsogoleri wochokera ku fuko la Manase, mwana wa Yosefe;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa ana a Yosefe; wa pfuko la ana a Manase, kalonga Haniyeli mwana wa Efodi.