Numbers 34:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'fuko la ana a Isakara akhale Palatiele mwana wa Azani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palitieli mwana wa Azani, mtsogoleri wochokera ku fuko la Isakara,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa pfuko la ana a Isakara, kalonga Palitiyeli mwana wa Azana.