Numbers 34:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa ndiwo amene Chauta adalamula kuti agaŵe choloŵa cha Aisraele m'dziko la Kanani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israele cholowa chao m'dziko la Kanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndiwo mayina a anthu amene Yehova analamula kuti agawe cholowa cha Aisraeli mʼdziko la Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israyeli colowa cao m'dziko la Kanani.