Numbers 35:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti: Pamene muwoloka mtsinje wa Yordani ndi kuloŵa m'dziko la Kanani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pakuoloka inu Yordani kulowa m'dziko la Kanani,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yankhula ndi Aisraeli kuti, ‘Pamene muwoloka Yorodani kulowa mu Kanaani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenandi ana a Israyeli, nuti nao, Pakuoloka inu Yordano kulowa m'dziko la Kanani,