Numbers 35:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzapereke mizinda itatu patsidya la kuvuma la mtsinje wa Yordani, ndi mizinda itatu m'dziko la Kanani, kuti ikhale mizinda yothaŵirako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mupereke midzi itatu tsidya lino la Yordani, ndi midzi itatu mupereke m'dziko la Kanani, ndiyo yopulumukirako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mupereke itatu mbali ino ya Yorodani ndi itatu ina mu Kanaani kuti ikhale mizinda yopulumukirako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mupereke midzi itatu tsidya lino la Yordano, ndi midzi itatu mupereke m'dziko la Kanani, ndiyo yopulumukirako.