Numbers 35:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbale wake wa munthu wakufayo ndiye adzaphe wopha mnzakeyo. Akadzangokumana, wopha mnzakeyo adzamuphe ndi munthu wolipsira magaziyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolipsa mwazi mwini wake aphe wakupha munthuyo; pakumpeza amuphe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolipsira adzamuphanso wakuphayo. Pamene akumana naye adzayenera kumupha ndithu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolipsa mwazi mwini wace aphe wakupha munthuyo; pakumkumika amuphe,