Numbers 35:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma ngati munthu abaya mnzake mwangozi osati chifukwa cha chidani, kapena alasa mnzake ndi chida osamubisalira,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akampyoza modzidzimuka, osamuda, kapena kumponyera kanthu osamlalira,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Koma ngati popanda udani wina uliwonse, mwadzidzidzi akankha wina kapena kumuponyera chinthu osati mwadala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akampyoza modzidzimuka, osamuda, kapena kumponyera kanthu osamialira,