Numbers 35:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kapena amulasa ndi mwala woti nkupha munthu, koma amlasa osamuwona mnzakeyo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wake, kapena womfunira choipa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena mosamuona nʼkumuponyera mwala womwe utha kumupha, munthuyo nʼkufa, tsono pakuti sanali mdani wake ndipo sanaganizire zomupweteka,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wace, kapena womfunira coipa;