Numbers 35:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati munthu wopha mnzake mwangoziyo atuluka nthaŵi iliyonse kunja kwa malire a mzinda umene adathaŵiramo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wakupha munthu akatuluka nthawi iliyonse kulumpha malire a mudzi wake wopulumukirako kumene anathawirako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Koma ngati wolakwayo atuluka kunja kwa malire a mzinda wopulumukirako kumene anathawira
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wakupha munthu akaturuka nthawi iri yonse kulumpha malire a mudzi wace wopulumukirako kumene anathawirako;