Numbers 35:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo mbale wa munthu wakufa uja ampeza ali kunja kwa malire a mzindawo, nkupha wopha mnzake uja, sadzapalamula mlandu wopha munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakampeza wolipsa mwazi kunja kwa malire a mudzi wake wothawirako, ndipo wolipsa mwazi akapha wakupha munthu, alibe kuchimwira mwazi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo wobwezera choyipa nʼkumupeza kunja kwa mzindawo, wolipsirayo atha kumupha wolakwayo popanda kugamula mlandu wakupha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakampeza wolipsa mwazi kunja kwa malire a mudzi wace wothawirako, ndipo wolipsa mwazi akapha wakupha munthu, alibe kucimwira mwazi;