Numbers 35:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati wina aliyense apha mnzake, wopha mnzakeyo ayenera kuphedwa, mboni zitapereka umboni wao. Koma munthu asaphedwe pamene munthu mmodzi yekha wapereka umboni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aliyense wakantha munthu, wakupha munthuyo aziphedwa pakamwa pa mboni; koma mboni ya munthu mmodzi isafikire kuti munthu afe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Aliyense wopha munthu ayeneranso kuphedwa ngati pali umboni okwanira. Koma wina asaphedwe ngati pali mboni imodzi yokha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ali yense wakantha munthu, wakupha munthuyo aziphedwa pakamwa pa mboni; koma mboni ya munthu mmodzi isafikire kuti munthu afe.