Numbers 35:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo musalandire dipo loombolera munthu amene ali mu mzinda wake wothaŵirako kuti abwerere ndi kukakhala ku dziko lake, mkulu wa ansembeyo asanamwalire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamalandira dipo lakuombola iye amene adathawira kumudzi wake wopulumukirako, kuti abwerenso kukhala m'dziko, kufikira atafa mkulu wa ansembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Simuyeneranso kulandira dipo kwa munthu amene wathawira ku mzinda wopulumikirako kuti wothawayo abwerere kwawo, pokhapokha ngati mkulu wa ansembe wamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamalandira dipo lakuombola iye amene adathawira ku mudzi wace wopulumukirako, kuti abwerenso kukhala m'dziko, kufikira atafa wansembe.