Numbers 36:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mala, Tiriza, Hogola, Milika ndi Nowa, ana aakazi a Zelofehadi, adakwatiwa ndi ana a abale a bambo wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza Mala, Tiriza, ndi Hogila, ndi Milika, ndi Nowa, ana akazi a Zelofehadi, anakwatibwa ndi ana amuna a abale a atate wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aakazi a Zelofehadi amene ndi Mahila, Tiriza, Hogila, Milika ndi Nowa, anakwatiwa ndi asuweni awo a ku mbali ya abambo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popeza Mala, Tiriza, ndi Hogila, ndi Milika, ndi Nowa, ana akazi a Tselofekadi, anakwatibwa ndi ana amuna a abale a atate wao.