Numbers 36:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Mose adaŵalamula Aisraele potsata mau a Chauta, adati, “Zimene akunena ana a Yosefezi nzoona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose analamulira ana a Israele monga mwa mau a Yehova, nati, Fuko la ana a Yosefe linena zoona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mwa lamulo la Yehova, Mose anapereka lamulo ili kwa Aisraeli: “Zimene ana a Yosefe akunena ndi zoona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose analamulira ana a Israyeli monga mwa mau a Yehova, nati, Pfuko la ana a Yosefe linena zaona.