Numbers 4:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musalole kuti a m'banja la Kohati aonongeke pakati pa Alevi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamasadza fuko la mabanja a Kohati kuwachotsa pakati pa Alevi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Onetsetsani kuti mabanja a fuko la Kohati asachotsedwe kwa Alevi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamasadza pfuko la mabanja a Kohati kuwacotsa pakati pa Alevi;