Numbers 4:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene mabanja a Geresoni ayenera kuchita, ndiponso zimene ayenera kumanyamula ndi izi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ntchito ya mabanja a Ageresoni, pogwira ntchito ndi kusenza katundu ndi iyi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ntchito ya mafuko a Ageresoni pamene akugwira ntchito ndi kunyamula katundu ndi iyi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nchito ya mabanja a Agerisoni, pogwira nchito ndi kusenza katundu ndi iyi;