Numbers 4:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uŵerenge amuna kuyambira a zaka makumi atatu mpaka a zaka makumi asanu, aliyense amene angathe kutumikira m'chihema chamsonkhano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uwawerenge kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuchita ntchito ya chihema chokomanako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Werenga amuna onse a zaka makumi atatu mpaka zaka makumi asanu zakubadwa amene akatumikire mu tenti ya msonkhano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uwawerenge kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kucita nchito ya cihema cokomanako.