Numbers 4:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuyambira anthu a zaka makumi atatu mpaka makumi asanu, onse amene ankatha kutumikira m'chihema chamsonkhano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuti agwire ntchito m'chihema chokomanako,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amuna onse a zaka makumi atatu mpaka makumi asanu amene anabwera kudzagwira ntchito ku tenti ya msonkhano,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa utumikiwu, kuti agwire nchito m'cihema cokomanako,