Numbers 4:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuyambira anthu a zaka makumi atatu mpaka a zaka makumi asanu, onse amene ankatha kugwira ntchito yotumikira ndi yonyamula katundu wa m'chihema chamsonkhano,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa kugwira ntchito ya utumikiwu, ndiyo ntchito ya akatundu m'chihema chokomanako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aamuna onse a zaka makumi atatu mpaka zaka makumi asanu omwe anabwera kudzagwira ntchito yonyamula zinthu ku tenti ya msonkhano
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu kufikira a zaka makumi asanu, onse akulowa kugwira nchito ya utumikiwu, ndiyo nchito ya akatundu m'cihema cokomanako;