Numbers 5:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati udamzemberapo mwamuna wako, ngakhale kuti unali m'manja mwake, nudziipitsa, ndipo ngati udagona ndi mwamuna wina wosakhala mwamuna wako,’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwe, ngati wapatukira mwamuna wako, ngati wadetsedwa, kuti wagona nawe munthu, wosati mwamuna wako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati wayenda njira yoyipa uli pa ukwati ndi mwamuna wako ndi kudzidetsa pogonana ndi mwamuna amene si mwamuna wako,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwe, ngati wapatukira mwamuna wako, ngati wadetsedwa, kuti wagona nawe munthu, wosati mwamuna wako;