Numbers 5:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo wansembe achotse m'manja mwa mkaziyo chopereka cha chakudya choperekera nsanje ija. Aipereke moweyula pamaso pa Chauta, ndipo abwere nayo ku guwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wansembe atenge nsembe yaufa yansanje m'manja mwa mkazi, naweyule nsembe yaufa pamaso pa Yehova, nabwere nayo ku guwa la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe achotse mʼmanja mwa mkaziyo nsembe yachakudya ya nsanje ija, nayiweyula pamaso pa Yehova ndi kuyipereka pa guwa lansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wansembe atenge nsembe yaufa m'manja mwa mkazi, naweyule nsembe yaufa pamaso pa Yehova, nabwere nayo ku guwa la nsembe.