Numbers 5:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mkaziyo akakhala kuti sadadziipitse ndipo alibe tchimo, adzakhala wopanda mlandu, ndipo azidzabala ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati mkazi sanadetsedwe, nakhala woyera, pamenepo adzapulumuka, nadzaima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati mkaziyo sanadzidetse ndi kuti alibe tchimo, adzakhala wopanda mlandu ndipo adzabereka ana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati mkazi sanadetsedwa, nakhala woyera, pamenepo adzapulumuka, nadzaima.

Recommended Reading