Numbers 5:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti, mwamuna kapena mkazi akachita munthu mnzake choipa chilichonse chimene anthu amati wochita zotere ndi wosakhulupirika kwa Chauta, munthuyo ndi wochimwadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi ana a Israele, ndi kuti Mwamuna kapena mkazi akachita tchimo lililonse amachita anthu, kuchita mosakhulupirika pa Yehova, nakapalamuladi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Uza Aisraeli kuti, ‘Pamene mwamuna kapena mayi walakwira mnzake mwa njira iliyonse, ndiye kuti ndi wosakhulupirika pamaso pa Yehova. Munthuyo ndi wochimwa ndithu ndipo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nena ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Mwamuna kapena mkazi akacita cimo liri lonse amacita anthu, kucita mosakhulupirika pa Yehova, nakaparamuladi;