Numbers 6:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku onse pamene munthuyo ali wodzipereka kwa Chauta, asadye chilichonse chochokera ku mphesa, ngakhale mbeu zake kapena makungu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku onse a kusala kwake asadye kanthu kopangika ndi mphesa, kuyambira nthanga zake kufikira khungu lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi yonse imene ali Mnaziri, asamadye chilichonse chopangidwa kuchokera ku mphesa ngakhale mbewu zake kapena makungu ake.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku onse a kusala kwace asadye kanthu kopangika ndi mphesa, kuyambira nthanga zace kufikira khungu lace,