Numbers 7:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lachitatu linali la Eliyabu mwana wa Heloni mtsogoleri wa Azebuloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachitatu kalonga wa ana a Zebuloni, ndiye Eliyabu mwana wa Heloni:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachitatu, Eliabu mwana wa Heloni, mtsogoleri wa Azebuloni, anabweretsa chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacitatu kalonga wa ana a Zebuloni, ndiye Eliyabu mwana wa Heloni: