Numbers 7:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lachinai linali la Elizuri mwana wa Sedeuri, mtsogoleri wa Arubeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachinai Elizuri, mwana wa Sedeuri, kalonga wa ana a Rubeni:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lachinayi linali la Elizuri mwana wa Sedeuri, mtsogoleri wa fuko la Rubeni, anabweretsa chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacinai Elizuri, mwana wa Sedeuri, kalonga wa ana a Rubeni: