Numbers 7:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lachisanu ndi chimodzi linali la Eliyasafu mwana wa Deuwele mtsogoleri wa Agadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachisanu ndi chimodzi kalonga wa ana a Gadi, Eliyasafu mwana wa Deuwele:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachisanu ndi chimodzi, Eliyasafu mwana wa Deuweli, mtsogoleri wa fuko la Gadi, anabweretsa chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacisanu ndi cimodzi, kalonga wa ana a Gadi, Eliyasafe mwana wa Deyueli: