Numbers 7:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ulandire zimenezi kwa anthuwo kuti zithandize potumikira m'chihema chamsonkhano. Uŵapatse Alevi zimenezo, aliyense zoyenera ntchito yake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakuchitira ntchito ya chihema chokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa ntchito yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ulandire zimenezi kwa iwo kuti zigwire ntchito ku tenti ya msonkhano. Uzipereke kwa Alevi, aliyense monga mwa ntchito yake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uzilandira kwa iwo, kuti zikhale zakucitira nchito ya cihema cokomanako; nuzipereke kwa Alevi, yense monga mwa nchito yace.