Numbers 7:66 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lakhumi linali la Ahiyezere mwana wa Amishadai, mtsogoleri wa Adani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezere mwana wa Amisadai:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lakhumi Ahiyezeri mwana wa Amisadai, mtsogoleri wa fuko la Dani anabweretsa chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lakhumi kalonga wa ana a Dani, ndiye Ahiyezeri mwana wa Amisadai: