Numbers 7:72 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku la 11 linali la Pagiyele mwana wa Okarani, mtsogoleri wa fuko la Asere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku la khumi ndi chimodzi, Pagieli mwana wa Okirani, mtsogoleri wa fuko la Aseri, anabweretsa chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Aseri, ndiye Pagiyeli mwana wa Okirani;