Numbers 7:78 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku la 12 linali la Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa Anafutali,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lakhumi ndi chiwiri kalonga wa ana a Nafutali, ndiye Ahira mwana wa Enani:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku la khumi ndi chimodzi Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa fuko la Nafutali, anabweretsa chopereka chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lakhumi ndi ciwiri kalonga wa ana a Nafitali, ndiye Ahira mwana wa Enani: