Numbers 8:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ntchito za Alevi ndi izi: kuyambira anthu a zaka 25 ndi opitirirapo, azipita kukagwira ntchito yotumikira m'chihema chamsonkhano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi cha Alevi: kuyambira ali wa zaka makumi awiri ndi zisanu ndi mphambu azilowa kutumikira utumikiwu mu ntchito ya chihema chokomanako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ntchito za Alevi ndi izi: Amuna a zaka 24 kapena kuposera pamenepa ndiye azibwera kudzagwira ntchito ku tenti ya msonkhano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi ca Alevi: kuyambira ali wa zaka makumi awiri ndi zisanu ndi mphambu azilowa kutumikira utumikiwu mu nchito ya cihema cokomanako;