Numbers 8:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akafika zaka makumi asanu aleke ntchito yotumikira, ndipo asatumikirenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo kuyambira zaka makumi asanu azileka kutumikira utumikiwu, osachitanso ntchitoyi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma akakwana zaka makumi asanu, apume pa ntchito yawo ya tsiku ndi tsiku ndi kulekeratu kugwira ntchitoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo kuyambira zaka makumi asanu azileka kutumikira utumikiwu, osacitanso nchitoyi;