Obadiah 1:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuuza Aedomu kuti, “Ndithu ndidzakutsitsani kotheratu, anthu a mitundu yonse adzakunyozani kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, ndakuika wamng'ono mwa amitundu; unyozedwa kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Taona, ndidzakuchepetsani pakati pa anthu a mitundu ina; udzanyozedwa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, ndakuika wamng'ono mwa amitundu; unyozedwa kwambiri.