Obadiah 1:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngwazi zochokera ku Yerusalemu zidzagonjetsa ndi kumalamulira dziko la Edomu ndipo ufumu wonse udzakhala wa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo apulumutsi adzakwera pa phiri la Ziyoni kuweruza phiri la Esau; ndipo ufumu udzakhala wake wa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Opulumukawo adzapita ku Phiri la Ziyoni ndipo adzalamulira mapiri a Esau. Koma ufumuwo udzakhala wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo apulumutsi adzakwera pa phiri la Ziyoni kuweruza phiri la Esau; ndipo ufumu udzakhala wace wa Yehova.