Obadiah 1:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani m'mene alisakazira dziko la Esau, ndi m'mene achifunkhira chuma chake chonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Za Esau zasanthulidwa; ha! Zobisika zake zafunidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Esau adzalandidwa zinthu zonse, chuma chake chobisika chidzabedwa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! za Esau zasanthulidwa; ha! zobisika zace zafunidwa.