Obadiah 1:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ogwirizana nanu akunyengani, akupirikitsani m'dziko mwanu. Okuthandizani pa nkhondo akugonjetsani. Abwenzi anu apamtima akutcherani msampha, mwathedwa nzeru tsopano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu onse a akupangana nawe anakuperekeza mpaka pamalire; anthu okhala ndi mtendere nawe anakunyenga, nakuposa mphamvu; iwo akudya chakudya chako akutchera msampha pansi pako; mulibe nzeru mwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse ogwirizana nawo adzakupirikitsira kumalire; abwenzi ako adzakunyenga ndi kukugonjetsa; amene amadya chakudya chako adzakutchera msampha, koma iwe sudzazindikira zimenezi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu onse a akupangana nawe anakuperekeza mpaka pamalire; anthu okhala ndi mtendere nawe anakunyenga, nakuposa mphamvu; iwo akudya cakudya cako akuchera msampha pansi pako; mulibe nzeru mwa iye.